Yeremiya 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndinayangʼana ndipo ndinaona kuti munda wa zipatso unali utasanduka thengo,Komanso mizinda yake yonse inali itagwetsedwa.+ Zimenezi zinachitika chifukwa cha Yehova,Chifukwa cha mkwiyo wake woyaka moto.
26 Ndinayangʼana ndipo ndinaona kuti munda wa zipatso unali utasanduka thengo,Komanso mizinda yake yonse inali itagwetsedwa.+ Zimenezi zinachitika chifukwa cha Yehova,Chifukwa cha mkwiyo wake woyaka moto.