Yeremiya 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa cha phokoso la asilikali okwera pamahatchi ndiponso oponya mivi ndi uta,Mzinda wonse wathawa.+ Alowa paziyangoyango,Ndipo akwera mʼmatanthwe.+ Mumzinda uliwonse anthu athawamoNdipo palibe munthu amene akukhalamo.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:29 Kukambitsirana, tsa. 357
29 Chifukwa cha phokoso la asilikali okwera pamahatchi ndiponso oponya mivi ndi uta,Mzinda wonse wathawa.+ Alowa paziyangoyango,Ndipo akwera mʼmatanthwe.+ Mumzinda uliwonse anthu athawamoNdipo palibe munthu amene akukhalamo.”