Yeremiya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzapita kwa anthu olemekezeka nʼkulankhula nawo,Chifukwa mosakayikira akuyenera kudziwa njira ya Yehova,Zimene Mulungu wawo amafuna.+ Koma onsewo athyola goli la MulunguNdipo adula zingwe za Mulungu.”
5 Ndidzapita kwa anthu olemekezeka nʼkulankhula nawo,Chifukwa mosakayikira akuyenera kudziwa njira ya Yehova,Zimene Mulungu wawo amafuna.+ Koma onsewo athyola goli la MulunguNdipo adula zingwe za Mulungu.”