Yeremiya 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi ndingakukhululukire bwanji zinthu zimenezi? Ana ako aamuna andisiya,Ndipo amalumbira pa zinthu zimene si Mulungu.+ Ndinkawapatsa zimene ankafunikira,Koma anapitiriza kuchita chigololo,Ndipo ankapita kunyumba ya hule mʼchigulu.
7 Kodi ndingakukhululukire bwanji zinthu zimenezi? Ana ako aamuna andisiya,Ndipo amalumbira pa zinthu zimene si Mulungu.+ Ndinkawapatsa zimene ankafunikira,Koma anapitiriza kuchita chigololo,Ndipo ankapita kunyumba ya hule mʼchigulu.