-
Yeremiya 5:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 “Kodi sindikuyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” akutero Yehova.
“Kodi sindikuyenera kubwezera mtundu wa anthu oterewa?
-