-
Yeremiya 6:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 “Choncho tamverani, inu mitundu ya anthu,
Kuti mudziwe anthu inu,
Zimene zidzachitikire anthu a ku Yerusalemu.
-