20 “Kodi lubani wochokera ku Sheba
Komanso bango lonunkhira lochokera kudziko lakutali zimene mukundibweretsera, zili ndi phindu lanji kwa ine?
Nsembe zanu zopsereza zathunthu nʼzosavomerezeka,
Ndipo nsembe zanu zina zonse zimene mukupereka sizikundisangalatsa.”+