Yeremiya 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Sinthani njira zanu komanso zochita zanu ndipo muzichita zabwino. Mukatero ine ndidzakulolani kuti mupitirize kukhala mʼdziko lino.+
3 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Sinthani njira zanu komanso zochita zanu ndipo muzichita zabwino. Mukatero ine ndidzakulolani kuti mupitirize kukhala mʼdziko lino.+