Yeremiya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iwe usawapempherere anthu awa. Usafuule kwa ine, kuwapempherera kapena kundichonderera kuti ndiwathandize,+ chifukwa ine sindidzakumvetsera.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:16 Yeremiya, tsa. 139 Nsanja ya Olonda,12/1/2001, ptsa. 30-31
16 Koma iwe usawapempherere anthu awa. Usafuule kwa ine, kuwapempherera kapena kundichonderera kuti ndiwathandize,+ chifukwa ine sindidzakumvetsera.+