-
Yeremiya 8:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 “Pa nthawi imeneyo,” akutero Yehova, “mafupa a mafumu a Yuda, a akalonga awo, a ansembe, a aneneri ndi a anthu okhala mu Yerusalemu adzatulutsidwa mʼmanda awo.
-