-
Yeremiya 8:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 “Ndipo anthu onse otsala a banja loipali amene adzapulumuke adzaona kuti ndi bwino kufa kusiyana ndi kukhala ndi moyo, malo onse amene ndidzawabalalitsire,” akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-