-
Yeremiya 8:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 “Ndipo ukawauze kuti, ‘Yehova wanena kuti:
“Kodi munthu akagwa sadzukanso?
Ngati munthu mmodzi atabwerera, kodi winayo sangabwererenso?
-