Yeremiya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi munganene bwanji kuti: “Ndife anzeru, ndipo tili ndi chilamulo cha Yehova”?* Pamene zoona zake nʼzakuti zolembera zabodza+ za alembi zagwiritsidwa ntchito polemba zachinyengo.
8 Kodi munganene bwanji kuti: “Ndife anzeru, ndipo tili ndi chilamulo cha Yehova”?* Pamene zoona zake nʼzakuti zolembera zabodza+ za alembi zagwiritsidwa ntchito polemba zachinyengo.