Yeremiya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anayankha kuti: “Nʼchifukwa chakuti iwo asiya chilamulo changa chimene ndinawapatsa.* Komanso chifukwa chakuti sanatsatire chilamulocho ndiponso kumvera mawu anga.
13 Yehova anayankha kuti: “Nʼchifukwa chakuti iwo asiya chilamulo changa chimene ndinawapatsa.* Komanso chifukwa chakuti sanatsatire chilamulocho ndiponso kumvera mawu anga.