Yeremiya 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti,‘Chitani zinthu mozindikira. Itanani akazi oimba nyimbo zoimba polira kuti abwere.+Ndipo tumizani anthu kuti akaitane akazi odziwa kulira maliro,
17 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti,‘Chitani zinthu mozindikira. Itanani akazi oimba nyimbo zoimba polira kuti abwere.+Ndipo tumizani anthu kuti akaitane akazi odziwa kulira maliro,