Yeremiya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wanena kuti: “Musaphunzire miyambo ya anthu a mitundu ina,+Ndipo musachite mantha ndi zizindikiro zakumwamba,Chifukwa anthu a mitundu ina amachita mantha ndi zizindikirozo.+
2 Yehova wanena kuti: “Musaphunzire miyambo ya anthu a mitundu ina,+Ndipo musachite mantha ndi zizindikiro zakumwamba,Chifukwa anthu a mitundu ina amachita mantha ndi zizindikirozo.+