Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.