Yeremiya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye ndi Mulungu amene anapanga dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zake,Amene anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru zake.+Amenenso anatambasula kumwamba chifukwa cha kuzindikira kwake.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:12 Yandikirani, ptsa. 51-53
12 Iye ndi Mulungu amene anapanga dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zake,Amene anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru zake.+Amenenso anatambasula kumwamba chifukwa cha kuzindikira kwake.+