Yeremiya 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa Yehova wanena kuti: “Pa nthawi ino ndikuthamangitsa* anthu okhala mʼdzikoli,+Ndipo ndidzachititsa kuti akumane ndi mavuto.”
18 Chifukwa Yehova wanena kuti: “Pa nthawi ino ndikuthamangitsa* anthu okhala mʼdzikoli,+Ndipo ndidzachititsa kuti akumane ndi mavuto.”