Yeremiya 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsoka kwa ine chifukwa cha kuwonongedwa kwanga!*+ Bala langa ndi losachiritsika. Ndinanena kuti: “Ndithudi amenewa ndi matenda anga ndipo ndikufunika kuwapirira.
19 Tsoka kwa ine chifukwa cha kuwonongedwa kwanga!*+ Bala langa ndi losachiritsika. Ndinanena kuti: “Ndithudi amenewa ndi matenda anga ndipo ndikufunika kuwapirira.