-
Yeremiya 11:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Ulengeze mawu onsewa mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu kuti: ‘Imvani mawu a pangano langa ndipo muchite zimene mawuwo akunena.
-