-
Yeremiya 11:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Anthu a mu Yuda komanso okhala mu Yerusalemu akonza chiwembu choti andipandukire.
-