Yeremiya 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nʼchifukwa chiyani anthu anga okondedwa akupezekabe mʼnyumba yangaPamene ambiri a iwo akuchita zinthu zoipa? Kodi nyama yopatulika* idzawapulumutsa tsoka likadzawagwera? Kodi iwo adzasangalala pa nthawi imeneyo?
15 Nʼchifukwa chiyani anthu anga okondedwa akupezekabe mʼnyumba yangaPamene ambiri a iwo akuchita zinthu zoipa? Kodi nyama yopatulika* idzawapulumutsa tsoka likadzawagwera? Kodi iwo adzasangalala pa nthawi imeneyo?