-
Yeremiya 11:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mʼmbuyomu Yehova ankakutchulani kuti mtengo wa maolivi wa masamba obiriwira,
Wokongola komanso wobala zipatso.
Koma pamveka phokoso lamphamvu ndipo mtengowo wauyatsa moto,
Ndipo adani athyola nthambi zake.
-