Yeremiya 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Afesa tirigu koma akolola minga.+ Agwira ntchito yotopetsa koma osapeza phindu lililonse. Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawoChifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.”
13 Afesa tirigu koma akolola minga.+ Agwira ntchito yotopetsa koma osapeza phindu lililonse. Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawoChifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.”