-
Yeremiya 13:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma patapita masiku ambiri Yehova anandiuza kuti: “Nyamuka, pita kumtsinje wa Firate ndipo ukatenge lamba amene ndinakulamula kuti ukabise kumeneko.”
-