-
Yeremiya 13:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho ndinapita kumtsinje wa Firate ndipo ndinakumba pamalo amene ndinabisapo lambayo nʼkumutenga. Koma ndinaona kuti anali atawonongeka moti sakanagwiranso ntchito iliyonse.
-