-
Yeremiya 13:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 ‘Mofanana ndi mmene lamba amagwirira mʼchiuno mwa munthu, ine ndinachititsa nyumba yonse ya Isiraeli ndi nyumba yonse ya Yuda kundimamatira,’ akutero Yehova. ‘Ndinachita zimenezi kuti iwo akhale anthu anga,+ atchukitse dzina langa,+ anditamande ndi kukhala chinthu changa chokongola. Koma iwo sanandimvere.’+
-