Yeremiya 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kweza maso ako kuti uone anthu amene akubwera kuchokera kumpoto.+ Kodi ziweto zimene anakupatsa, nkhosa zako zokongola zija zili kuti?+
20 Kweza maso ako kuti uone anthu amene akubwera kuchokera kumpoto.+ Kodi ziweto zimene anakupatsa, nkhosa zako zokongola zija zili kuti?+