Yeremiya 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi udzanena chiyani chilango chako chikadzabweraKuchokera kwa anzako apamtima, amene unkagwirizana nawo kuchokera pa chiyambi?+ Kodi sudzamva zowawa za pobereka ngati za mkazi amene akubereka mwana?+
21 Kodi udzanena chiyani chilango chako chikadzabweraKuchokera kwa anzako apamtima, amene unkagwirizana nawo kuchokera pa chiyambi?+ Kodi sudzamva zowawa za pobereka ngati za mkazi amene akubereka mwana?+