Yeremiya 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ponena za anthu awa Yehova wanena kuti: “Iwo amakonda kumangoyendayenda+ ndipo samatha kudziletsa kuti asamayendeyende.+ Choncho Yehova sakusangalala nawo.+ Tsopano iye akumbukira zolakwa zawo ndipo awalanga chifukwa cha machimo awo.”+
10 Ponena za anthu awa Yehova wanena kuti: “Iwo amakonda kumangoyendayenda+ ndipo samatha kudziletsa kuti asamayendeyende.+ Choncho Yehova sakusangalala nawo.+ Tsopano iye akumbukira zolakwa zawo ndipo awalanga chifukwa cha machimo awo.”+