Yeremiya 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Usapempherere anthu awa kuti zinthu ziwayendere bwino.+