Yeremiya 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzawasandutsa chinthu chochititsa mantha kwa maufumu onse apadziko lapansi,+ chifukwa cha zimene Manase mwana wa Hezekiya, mfumu ya Yuda, anachita mu Yerusalemu.+
4 Ndidzawasandutsa chinthu chochititsa mantha kwa maufumu onse apadziko lapansi,+ chifukwa cha zimene Manase mwana wa Hezekiya, mfumu ya Yuda, anachita mu Yerusalemu.+