Yeremiya 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chuma chanu komanso zinthu zanu zamtengo wapatali ndidzazipereka kwa adani anu kuti azitenge.+Adzazitenga popanda malipiro chifukwa cha machimo anu onse amene munachita mʼdziko lanu lonse.
13 Chuma chanu komanso zinthu zanu zamtengo wapatali ndidzazipereka kwa adani anu kuti azitenge.+Adzazitenga popanda malipiro chifukwa cha machimo anu onse amene munachita mʼdziko lanu lonse.