Yeremiya 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Sindikhala pansi ndi gulu la anthu okonda zosangalatsa nʼkumasangalala nawo.+ Ndimakhala ndekha chifukwa dzanja lanu lili pa ine,Popeza mwandidzaza ndi mkwiyo.*+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:17 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 105/1/2004, ptsa. 11-128/15/1992, tsa. 17
17 Sindikhala pansi ndi gulu la anthu okonda zosangalatsa nʼkumasangalala nawo.+ Ndimakhala ndekha chifukwa dzanja lanu lili pa ine,Popeza mwandidzaza ndi mkwiyo.*+