Yeremiya 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Udzawayankhe kuti, ‘“Chifukwa chakuti makolo anu anandisiya,”+ akutero Yehova, “ndipo anapitiriza kutsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Koma ine anandisiya ndipo sanasunge malamulo anga.+
11 Udzawayankhe kuti, ‘“Chifukwa chakuti makolo anu anandisiya,”+ akutero Yehova, “ndipo anapitiriza kutsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Koma ine anandisiya ndipo sanasunge malamulo anga.+