Yeremiya 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Komabe masiku akubwera,’ akutero Yehova, ‘pamene sadzalumbiranso kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa Aisiraeli mʼdziko la Iguputo!”+
14 ‘Komabe masiku akubwera,’ akutero Yehova, ‘pamene sadzalumbiranso kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa Aisiraeli mʼdziko la Iguputo!”+