-
Yeremiya 16:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 ‘Ine ndikuitana asodzi ambiri,’ akutero Yehova,
‘Ndipo adzawawedza.
Kenako ndidzaitana anthu ambiri osaka nyama,
Ndipo adzawasaka mʼphiri lililonse, pachitunda chilichonse,
Komanso mʼmapanga a mʼmatanthwe.
-