-
Yeremiya 16:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 “Choncho ine ndiwaphunzitsa.
Pa nthawi ino ndiwachititsa kuti adziwe mphamvu ndi nyonga zanga,
Ndipo adziwa kuti dzina langa ndine Yehova.”
-