-
Yeremiya 17:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 “Tchimo la Yuda lalembedwa ndi chitsulo chogobera.
Lalembedwa ndi cholembera cha dayamondi mʼmitima yawo
Ndi panyanga za maguwa awo ansembe.
-