-
Yeremiya 17:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma ine sindinaleke kukutsatirani monga mʼbusa wanu,
Kapena kulakalaka tsiku latsoka.
Inu Mulungu, mukudziwa bwino zimene pakamwa panga panalankhula,
Chifukwa ndinalankhula pamaso panu.
-