Yeremiya 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Musamatulutse katundu aliyense mʼnyumba zanu pa tsiku la Sabata ndipo musamagwire ntchito iliyonse.+ Muziona kuti tsiku la Sabata ndi lopatulika mogwirizana ndi zimene ndinalamula makolo anu.+
22 Musamatulutse katundu aliyense mʼnyumba zanu pa tsiku la Sabata ndipo musamagwire ntchito iliyonse.+ Muziona kuti tsiku la Sabata ndi lopatulika mogwirizana ndi zimene ndinalamula makolo anu.+