Yeremiya 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzawamwaza pamaso pa adani awo ngati mmene mphepo yochokera kumʼmawa imamwazira fumbi. Sindidzawaonetsa nkhope yanga, koma ndidzawafulatira pa tsiku la tsoka lawo.”+
17 Ndidzawamwaza pamaso pa adani awo ngati mmene mphepo yochokera kumʼmawa imamwazira fumbi. Sindidzawaonetsa nkhope yanga, koma ndidzawafulatira pa tsiku la tsoka lawo.”+