-
Yeremiya 20:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Tsopano Pasuri, mwana wa Imeri, wansembe, amenenso anali mtumiki wamkulu mʼnyumba ya Yehova, ankamvetsera pamene Yeremiya ankalosera zinthu zimenezi.
-