-
Yeremiya 20:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chifukwa Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikukuchititsa kuti ukhale chinthu chochititsa mantha kwa iwe ndi kwa anzako onse, ndipo adzaphedwa ndi lupanga la adani awo iweyo ukuona.+ Anthu onse a mu Yuda ndidzawapereka mʼmanja mwa mfumu ya ku Babulo. Ena adzapita nawo ku Babulo ndipo ena adzawapha ndi lupanga.+
-