-
Yeremiya 20:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Munthu ameneyo akhale ngati mizinda imene Yehova anaigonjetsa popanda kuimvera chisoni.
Mʼmawa kwambiri azimva kulira kofuula ndipo masana azimva phokoso lochenjeza.
-