-
Yeremiya 21:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 ‘Iwe amene umakhala mʼchigwa, ine ndakuukira,
Iwe thanthwe limene lili pamalo afulati,’ akutero Yehova.
‘Koma inu amene mukunena kuti: “Kodi ndi ndani amene adzabwere kuno kuti atiukire?
Ndipo ndi ndani amene adzabwere mʼmalo athu okhala?”
-