-
Yeremiya 22:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Munthu wakufa musamulire,
Ndipo musamumvere chisoni.
Mʼmalomwake, mulirire kwambiri munthu amene watengedwa kupita kudziko lina,
Chifukwa sadzabwereranso kudzaona dziko limene anabadwira.
-