-
Yeremiya 22:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ankateteza anthu ovutika komanso osauka pa mlandu,
Moti zinthu zinkayenda bwino.
‘Kodi kumeneku sindiye kundidziwa?’ akutero Yehova.
-