Yeremiya 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Inu amene mumakhala mu Lebanoni,+Amene mukukhala mʼnyumba zamitengo ya mkungudza,+Mudzabuula kwambiri mukadzayamba kumva zowawa,Mukadzayamba kumva ululu* ngati wa mkazi amene akubereka.+
23 Inu amene mumakhala mu Lebanoni,+Amene mukukhala mʼnyumba zamitengo ya mkungudza,+Mudzabuula kwambiri mukadzayamba kumva zowawa,Mukadzayamba kumva ululu* ngati wa mkazi amene akubereka.+